Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 26:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 “Werengani Aisraeli onse mwa mabanja awo, onse a zaka makumi awiri kapena kuposera pamenepo omwe angathe kugwira ntchito ya usilikali mʼgulu lankhondo la Israeli.”

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

2 Werenga khamu lonse la ana a Israele, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, monga mwa nyumba za makolo ao, onse akutulukira kunkhondo mu Israele.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Werenga khamu lonse la ana a Israele, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, monga mwa nyumba za makolo ao, onse akutulukira kunkhondo m'Israele.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 “Uchite chiŵerengero cha mpingo wonse wa Aisraele, kuyambira anthu aamuna a zaka makumi aŵiri ndi opitirirapo, potsata mabanja a makolo ao, anthu onse a m'dziko la Israele amene angathe kumenya nkhondo.”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:2
3 Mawu Ofanana  

Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa