Filemoni 1:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 komabe ndikupempha mwachikondi. Ine Paulo, munthu wokalamba, ndipo tsopano ndili mʼndende chifukwa cha Khristu Yesu, Onani mutuwoBuku Lopatulika9 koma makamaka ndidandaulira mwa chikondi, pokhala wotere, Paulo nkhalamba, ndipo tsopano wandendenso wa Khristu Yesu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 koma makamaka ndidandaulira mwa chikondi, pokhala wotere, Paulo nkhalamba, ndipo tsopano wandendenso wa Khristu Yesu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Komabe chifukwa cha chikondi makamaka ndingochita kukupempha, ine Paulo amene ndili nkhalamba, amenenso ndili m'ndende tsopano chifukwa cha Khristu Yesu. Onani mutuwo |