Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 2:1 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Ndipo munthu wina wa fuko la Levi anakwatira mkazi wa fuko lomwelo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

1 Ndipo anamuka munthu wa banja la Levi, natenga mwana wamkazi wa Levi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo anamuka munthu wa banja la Levi, natenga mwana wamkazi wa Levi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Munthu wina wa fuko la Levi adakwatira mkazi wa fuko lomwelo.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 2:1
6 Mawu Ofanana  

Israeli akanali mʼderali, Rubeni anapita nakagonana ndi Biliha, mdzakazi wa abambo ake. Yakobo uja anazimva zimenezi. Yakobo anali ndi ana aamuna khumi ndi awiri:


Koma Hadadi akanali mwana anathawira ku Igupto pamodzi ndi akuluakulu ena a ku Edomu amene ankatumikira abambo ake.


Dzina la mkazi wa Amramu linali Yokobedi, mdzukulu wa Levi, yemwe anabadwa mwa Alevi mu Igupto. Yokobedi anaberekera Amramu Aaroni, Mose ndi Miriamu mlongo wawo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa