Danieli 7:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndipo mʼnyangayo munatuluka zirombo zazikulu zinayi, chilichonse chosiyana ndi chinzake. Onani mutuwoBuku Lopatulika3 Ndipo zinatuluka m'nyanja zilombo zazikulu zinai zosiyanasiyana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo zinatuluka m'nyanja zilombo zazikulu zinai zosiyanasiyana. Onani mutuwo |
Chirombo chimene wachionachi chinalipo kale koma tsopano kulibe ndipo chidzatuluka ku chidzenje chakuya ndi kupita kukawonongedwa. Anthu okhala pa dziko lapansi amene mayina awo sanalembedwe mʼbuku lamoyo kuyambira pa kulengedwa kwa dziko lapansi adzadabwa pamene adzaona chirombocho, chifukwa chinalipo kale, tsopano kulibe, komabe chidzabwera.