Danieli 7:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo zinatuluka m'nyanja zilombo zazikulu zinai zosiyanasiyana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo zinatuluka m'nyanja zilombo zazikulu zinai zosiyanasiyana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndipo mʼnyangayo munatuluka zirombo zazikulu zinayi, chilichonse chosiyana ndi chinzake. Onani mutuwo |
Chilombo chimene unachiona chinaliko, koma kulibe; ndipo chidzatuluka m'chiphompho chakuya, ndi kunka kuchitayiko. Ndipo adzazizwa iwo akukhala padziko amene dzina lao silinalembedwe m'buku la moyo chiyambire makhazikidwe a dziko lapansi, pakuona chilombo, kuti chinaliko, ndipo kulibe, ndipo chidzakhalako.