Danieli 2:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 mfumuyo inawawuza kuti, “Ndalota loto lomwe likundisautsa ndipo ndikufuna kudziwa tanthauzo lake.” Onani mutuwoBuku Lopatulika3 Niti nao mfumu, Ndalota loto, nuvutika mzimu wanga kudziwa lotolo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Niti nao mfumu, Ndalota loto, nuvutika mzimu wanga kudziwa lotolo. Onani mutuwo |