Danieli 2:1 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Chaka chachiwiri cha ulamuliro wake, Nebukadinezara analota maloto; anavutika mu mtima mwake ndipo analephera kugona. Onani mutuwoBuku Lopatulika1 Chaka chachiwiri cha Nebukadinezara mfumu, Nebukadinezarayo analota maloto, ndi mzimu wake unavutika, ndi tulo take tidamwazikira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Chaka chachiwiri cha Nebukadinezara mfumu, Nebukadinezarayo analota maloto, ndi mzimu wake unavutika, ndi tulo take tidamwazikira. Onani mutuwo |