Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Danieli 1:16 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Choncho kapitawo anawachotsera chakudya ndi vinyo za ku nyumba yaufumu zija nawapatsa ndiwo zamasamba basi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

16 Pamenepo kapitaoyo anachotsa chakudya chao ndi vinyo akadamwa, nawapatsa zomera m'nthaka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Pamenepo kapitaoyo anachotsa chakudya chao ndi vinyo akadamwa, nawapatsa zomera m'nthaka.

Onani mutuwo Koperani




Danieli 1:16
2 Mawu Ofanana  

Ndipo Danieli anati kwa kapitawo amene anali mkulu wa nduna za mfumu amene anamuyika kuti ayangʼanire Danieli, Hananiya, Misaeli ndi Azariya,


“Chonde mutiyese ife akapolo anu pa masiku khumi: mutipatse masamba okha kuti tidye ndi madzi akumwa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa