Danieli 1:16 - Buku Lopatulika16 Pamenepo kapitaoyo anachotsa chakudya chao ndi vinyo akadamwa, nawapatsa zomera m'nthaka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Pamenepo kapitaoyo anachotsa chakudya chao ndi vinyo akadamwa, nawapatsa zomera m'nthaka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Choncho kapitawo anawachotsera chakudya ndi vinyo za ku nyumba yaufumu zija nawapatsa ndiwo zamasamba basi. Onani mutuwo |