Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 3:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Ana aamuna a Davide amene anabadwira ku Hebroni anali awa: Woyamba anali Amnoni, amayi ake anali Ahinoamu wa ku Yezireeli.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

2 Ndipo ana a Davide anabadwira ku Hebroni. Mwana woyamba ndiye Aminoni, wa Ahinowamu wa ku Yezireele;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo ana a Davide anabadwira ku Hebroni. Mwana woyamba ndiye Aminoni, wa Ahinowamu wa ku Yezireele;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Davide adabereka ana aamuna ku Hebroni. Mwana wake woyamba anali Aminoni, wobadwa kwa Ahinowamu wa ku Yezireele.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 3:2
6 Mawu Ofanana  

Munthu wolemerayo anali ndi nkhosa ndi ngʼombe zambiri,


Patapita zaka zinayi Abisalomu anati kwa mfumu, “Loleni ndipite ku Hebroni kuti ndikakwaniritse lonjezo limene ndinachita kwa Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa