2 Samueli 3:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo ana a Davide anabadwira ku Hebroni. Mwana woyamba ndiye Aminoni, wa Ahinowamu wa ku Yezireele; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo ana a Davide anabadwira ku Hebroni. Mwana woyamba ndiye Aminoni, wa Ahinowamu wa ku Yezireele; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Davide adabereka ana aamuna ku Hebroni. Mwana wake woyamba anali Aminoni, wobadwa kwa Ahinowamu wa ku Yezireele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ana aamuna a Davide amene anabadwira ku Hebroni anali awa: Woyamba anali Amnoni, amayi ake anali Ahinoamu wa ku Yezireeli. Onani mutuwo |