Zekariya 8:7 - Buku Lopatulika7 Atero Yehova wa makamu: Taonani, ndidzapulumutsa anthu anga m'dziko la kum'mawa, ndi m'dziko la kumadzulo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Atero Yehova wa makamu: Taonani, ndidzapulumutsa anthu anga m'dziko la kum'mawa, ndi m'dziko la kumadzulo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 “Ine Chauta Wamphamvuzonse ndikunena kuti, Ndidzapulumutsa anthu anga amene ali ku maiko akuvuma ndi akuzambwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Yehova Wamphamvuzonse akuti, “Taonani ndidzapulumutsa anthu anga kuchokera ku mayiko a kummawa ndi kumadzulo. Onani mutuwo |