Zekariya 8:5 - Buku Lopatulika5 Ndi m'miseu ya mzinda mudzakhala ana aamuna ndi aakazi akusewera m'miseu yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndi m'miseu ya mudzi mudzakhala ana aamuna ndi aakazi akusewera m'miseu yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ndipo m'miseu ya mumzindamo mudzadzaza ndi ana, anyamata ndi atsikana, amene azidzaseŵeramo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ndipo misewu ya mu mzindamo idzadzaza ndi anyamata ndi atsikana akusewera.” Onani mutuwo |
mudzamvekanso mau akukondwa ndi mau akusekera, mau a mkwati ndi mau a mkwatibwi, mau a iwo akuti, Myamikireni Yehova wa makamu, pakuti Yehova ndiye wabwino, chifundo chake nchosatha; ndi a iwo akutengera nsembe zoyamikira m'nyumba ya Yehova. Pakuti ndidzabweza undende wa dziko monga poyamba, ati Yehova.