Zekariya 8:11 - Buku Lopatulika11 Koma tsopano sindidzakhala kwa otsala a anthu awa monga momwe ndinakhalira masiku oyamba, ati Yehova wa makamu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Koma tsopano sindidzakhala kwa otsala a anthu awa monga momwe ndinakhalira masiku oyamba, ati Yehova wa makamu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Koma tsopano anthu atsalaŵa sindidzaŵachitanso zomwe ndidaaŵachita anthu kale. Ndikutero Ine Chauta Wamphamvuzonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Koma tsopano sindidzachitira otsala mwa anthu awa zomwe ndinachita kale,” akutero Yehova Wamphamvuzonse. Onani mutuwo |