Zekariya 6:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine, ndi kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine, ndi kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Kenaka Chauta adandipatsa uthenga wakuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Yehova anayankhula nane kuti, Onani mutuwo |