Zekariya 5:1 - Buku Lopatulika1 Pamenepo ndinakwezanso maso anga, ndinapenya, taonani, mpukutu wouluka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pamenepo ndinakwezanso maso anga, ndinapenya, taonani, mpukutu wouluka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ndidaonanso zinthu zina m'masomphenya: ndidaona chikalata chofutukula chikuuluka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ndinayangʼananso ndipo taonani ndinaona chikalata chimene chimawuluka. Onani mutuwo |