Zekariya 4:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo mthengayo adalankhula nane, anadzanso, nandiutsa ngati munthu woutsidwa m'tulo take. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo mthengayo adalankhula nane, anadzanso, nandiutsa ngati munthu woutsidwa m'tulo take. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Pambuyo pake mngelo amene ankalankhula nane uja adabweranso nandidzutsa monga momwe amadzutsira munthu amene ali m'tulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Kenaka mngelo amene amayankhula nane anabwerera nandidzutsa, ngati mmene amadzutsira munthu amene ali mʼtulo. Onani mutuwo |