Zefaniya 2:5 - Buku Lopatulika5 Tsoka, okhala m'dziko la kunyanja, mtundu wa Akereti! Mau a Yehova atsutsana nawe, Kanani, dziko la Afilisti; ndidzakuononga, kuti pasakhale wokhala m'dziko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Tsoka, okhala m'dziko la kunyanja, mtundu wa Akereti! Mau a Yehova atsutsana nawe, Kanani, dziko la Afilisti; ndidzakuononga, kuti pasakhale wokhala m'dziko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Tsoka kwa inu okhala m'mbali mwa nyanja, inu mtundu wa Akeretinu Mau a Chauta akukudzudzulani, inu anthu a ku Kanani, dziko la Afilisti, akuti, “Ndidzakuwonongani nonse sipadzatsala ndi mmodzi yemwe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Tsoka inu okhala mʼmbali mwa nyanja, inu mtundu wa Akereti; mawu a Yehova akutsutsa iwe Kanaani, dziko la Afilisti. “Ndidzakuwononga ndipo palibe amene adzatsale.” Onani mutuwo |