Zefaniya 2:4 - Buku Lopatulika4 Pakuti Gaza adzasiyidwa, ndi Asikeloni adzakhala bwinja; adzaingitsa Asidodi usana, ndi Ekeroni adzazulidwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Pakuti Gaza adzasiyidwa, ndi Asikeloni adzakhala bwinja; adzaingitsa Asidodi usana, ndi Ekeroni adzazulidwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mzinda wa Gaza udzasiyidwa, Asikeloni adzasanduka bwinja. Anthu a ku Asidodi adzapirikitsidwa masana mwadzidzidzi, Akeroni adzapasuka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Gaza adzasiyidwa ndipo Asikeloni adzasanduka bwinja. Nthawi yamasana Asidodi adzakhala wopanda anthu ndipo Ekroni adzazulidwa. Onani mutuwo |