Zefaniya 1:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo tsiku ilo ndidzalanga olumpha chiundo, nadzaza nyumba ya mbuye wao ndi chiwawa ndi chinyengo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo tsiku ilo ndidzalanga olumpha chiundo, nadzaza nyumba ya mbuye wao ndi chiwawa ndi chinyengo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pa tsiku limenelo ndidzalanga onse olumpha pa chiwundo, ndiponso amene amachita zankhanza ndi zonyenga zambiri.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pa tsiku limenelo ndidzalanga onse amene safuna kuponda pa chiwundo, amene amadzaza nyumba ya ambuye awo ndi chiwawa ndi chinyengo. Onani mutuwo |