Zefaniya 1:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo kudzachitika tsiku la nsembe ya Yehova, kuti ndidzalanga akalonga ndi ana a mfumu, ndi onse akuvala chovala chachilendo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo kudzachitika tsiku la nsembe ya Yehova, kuti ndidzalanga akalonga ndi ana a mfumu, ndi onse akuvala chovala chachilendo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Chauta akuti, “Pa tsiku limenelo la nsembe yanga ndidzalanga ana a mfumu ndi akalonga ake, ndi onse otengera zachilendo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Pa tsiku la nsembe ya Yehova ndidzalanga akalonga ndi ana aamuna a mfumu ndi onse amene amavala zovala zachilendo. Onani mutuwo |