Zefaniya 1:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo kudzachitika nthawi yomweyi kuti ndidzasanthula Yerusalemu ndi nyali, ndipo ndidzalanga amunawo okhala ndi nsenga, onena m'mtima mwao, Yehova sachita chokoma, kapena kuchita choipa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo kudzachitika nthawi yomweyi kuti ndidzasanthula Yerusalemu ndi nyali, ndipo ndidzalanga amunawo okhala ndi nsenga, onena m'mtima mwao, Yehova sachita chokoma, kapena kuchita choipa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pa nthaŵi imeneyo ndidzafufuzafufuza mu Yerusalemu ndi nyale, ndipo ndidzaŵalanga anthu ongokhala khale ngati vinyo wosakhutchumula, amene mumtima mwao amati, ‘Chauta sadzachitapo chabwino, kapena kuchitapo choipa.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pa nthawi imeneyo ndidzafufuzafufuza mu Yerusalemu ndi nyale ndi kulanga onse amene sakulabadira, amene ali ngati vinyo wosakhutchumulidwa, amene amaganiza kuti, ‘Yehova sadzachita chilichonse, chabwino kaya choyipa.’ Onani mutuwo |