Yuda 1:18 - Buku Lopatulika18 kuti ananena nanu, Pa nthawi yotsiriza padzakhala otonza, akuyenda monga mwa zilakolako zosapembedza za iwo okha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 kuti ananena nanu, Pa nthawi yotsiriza padzakhala otonza, akuyenda monga mwa zilakolako zosapembedza za iwo okha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Paja adakuuzani kuti, “Pa masiku otsiriza kudzafika anthu onyoza, otsata zilakolako zao zoipa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Iwo anakuwuzani kuti, “Mʼmasiku otsiriza kudzafika anthu onyoza, otsatira zofuna zawo zoyipa.” Onani mutuwo |