Yuda 1:19 - Buku Lopatulika19 Iwo ndiwo opatukitsa, anthu a makhalidwe achibadwidwe, osakhala naye Mzimu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Iwo ndiwo opatukitsa, anthu a makhalidwe achibadwidwe, osakhala naye Mzimu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Anthu ameneŵa ndi oyambitsa mipatuko. Amangotsata zapansipano, ndipo mumtima mwao alibe Mzimu Woyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Anthu amenewa ndi amene akubweretsa mipatuko pakati panu, amatsatira nzeru zachibadwa ndipo alibe Mzimu Woyera. Onani mutuwo |