Yuda 1:17 - Buku Lopatulika17 Koma inu, abale, mukumbukire mau onenedwa kale ndi atumwi a Ambuye wathu Yesu Khristu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Koma inu, abale, mukumbukire mau onenedwa kale ndi atumwi a Ambuye wathu Yesu Khristu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Koma inu okondedwa, muzikumbukira mau amene atumwi a Ambuye athu Yesu Khristu adaneneratu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Koma okondedwa, kumbukirani zimene atumwi a Ambuye athu Yesu Khristu ananeneratu. Onani mutuwo |