Yoweli 3:20 - Buku Lopatulika20 Koma Yuda adzakhala chikhalire, ndi Yerusalemu ku mibadwomibadwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Koma Yuda adzakhala chikhalire, ndi Yerusalemu ku mibadwomibadwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Koma ku Yudako kudzakhala anthu mpaka muyaya, ndipo ku Yerusalemu sikudzatha anthu pa mibadwo yonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Koma Yuda adzakhala ndi anthu mpaka muyaya ndi Yerusalemu ku mibadomibado. Onani mutuwo |