Yoweli 3:19 - Buku Lopatulika19 Ejipito adzasanduka bwinja, ndi Edomu adzasanduka chipululu chopanda kanthu, chifukwa cha chiwawachi anawachitira ana a Yuda; popeza anakhetsa mwazi wosachimwa m'dziko lao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ejipito adzasanduka bwinja, ndi Edomu adzasanduka chipululu chopanda kanthu, chifukwa cha chiwawachi anawachitira ana a Yuda; popeza anakhetsa mwazi wosachimwa m'dziko lao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 “Koma Ejipito adzasanduka chipululu, ndipo Edomu adzakhala bwinja lopanda anthu, chifukwa cha nkhondo imene adathira pa anthu a ku Yuda ndiponso chifukwa cha kukhetsa magazi a anthu osalakwa ku dziko lao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Koma Igupto adzasanduka bwinja, Edomu adzasanduka chipululu, chifukwa cha nkhondo imene anathira anthu a ku Yuda mʼdziko limene anakhetsa magazi a anthu osalakwa. Onani mutuwo |