Yoweli 2:9 - Buku Lopatulika9 Alumphira mzinda, athamanga palinga, akwerera nyumba, alowera pamazenera ngati khungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Alumphira mudzi, athamanga palinga, akwerera nyumba, alowera pamazenera ngati khungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Akuulumphira mzindawo, akukwera pamwamba pa malinga. Akuloŵa m'nyumba, akuloŵera pa windo ngati mbala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Amakhamukira mu mzinda, amathamanga mʼmbali mwa khoma. Amakwera nyumba ndi kulowamo; amalowera pa zenera ngati mbala. Onani mutuwo |