Yoweli 2:8 - Buku Lopatulika8 Sakankhana, ayenda lililonse m'mopita mwake; akagwa m'zida, siithyoka nkhondo yao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Sakankhana, ayenda lililonse m'mopita mwake; akagwa m'zida, siithyoka nkhondo yao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Sakukankhanakankhana, aliyense akuyenda molunjika. Akupyola pakati pa zida zankhondo, osaŵaimitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iwo sakankhanakankhana, aliyense amayenda molunjika. Amadutsa malo otchingidwa popanda kumwazikana. Onani mutuwo |