Yoweli 2:7 - Buku Lopatulika7 Athamanga ngati amphamvu; akwera linga ngati anthu a nkhondo; niliyenda lililonse njira yake, osasokonezeka m'mabande ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Athamanga ngati amphamvu; akwera linga ngati anthu a nkhondo; niliyenda lililonse njira yake, osasokonezeka m'mabande ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Akududuka ngati ankhondo. Akukwera malinga ngati asilikali. Aliyense akuyenda pa mzere, osasempha njira yake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Amathamanga ngati ankhondo; amakwera makoma ngati asilikali. Onse amayenda pa mizere, osaphonya njira yawo. Onani mutuwo |