Yoweli 2:6 - Buku Lopatulika6 Pamaso pao mitundu ya anthu ikumva zowawa, nkhope yonse zitumbuluka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Pamaso pao mitundu ya anthu ikumva zowawa, nkhope yonse zitumbuluka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Anthu a mitundu ina amachita mantha akaŵaona, nkhope zonse zimatumbuluka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Akangowaona, anthu a mitundu ina amazunzika mu mtima; nkhope iliyonse imagwa. Onani mutuwo |