Yoweli 2:5 - Buku Lopatulika5 Atumphako ngati mkokomo wa magaleta pamwamba pa mapiri, ngati kulilima kwa malawi a moto akupsereza ziputu, ngati mtundu wamphamvu wa anthu ondandalikira nkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Atumphako ngati mkokomo wa magaleta pamwamba pa mapiri, ngati kulilima kwa malawi a moto akupsereza ziputu, ngati mtundu wamphamvu wa anthu ondandalikira nkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Akulumpha pamwamba pa mapiri ndi phokoso longa la magaleta. Akumveka ngati malaŵi a moto otentha ziputu, ngati gulu lamphamvu lankhondo litakonzekera kumenya nkhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Akulumpha pamwamba pa mapiri ndi phokoso ngati la magaleta, ngati moto wothetheka wonyeketsa ziputu, ngati gulu lalikulu la ankhondo lokonzekera nkhondo. Onani mutuwo |