Yoweli 2:4 - Buku Lopatulika4 Maonekedwe ao aoneka ngati akavalo, nathamanga ngati akavalo a nkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Maonekedwe ao aoneka ngati akavalo, nathamanga ngati akavalo a nkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Maonekedwe ake ali ngati a akavalo, liŵiro lake ngati la akavalo ankhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Maonekedwe awo ali ngati akavalo; akuthamanga ngati akavalo ankhondo. Onani mutuwo |