Yoweli 1:9 - Buku Lopatulika9 Nsembe yaufa ndi nsembe yothira zalekeka kunyumba ya Yehova; ansembe, atumiki a Yehova, achita maliro. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Nsembe yaufa ndi nsembe yothira zalekeka kunyumba ya Yehova; ansembe, atumiki a Yehova, achita maliro. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Chopereka cha chakumwa ndi cha chakudya siziperekedwanso ku Nyumba ya Chauta. Ansembe akulira, atumiki a Chauta aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Chopereka cha chakudya ndi cha chakumwa sizikuperekedwa ku nyumba ya Yehova. Ansembe akulira, amene amatumikira pamaso pa Yehova. Onani mutuwo |