Yoweli 1:10 - Buku Lopatulika10 M'munda mwaonongeka, nthaka ilira; pakuti tirigu waonongeka, vinyo watsopano wamwelera, mafuta akudza pang'onong'ono. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 M'munda mwaonongeka, nthaka ilira; pakuti tirigu waonongeka, vinyo watsopano wamwelera, mafuta akudza pang'onong'ono. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Minda yaguga, nthaka ikulira poti tirigu waonongeka, mphesa zaumiratu, mitengo ya mafuta yauma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Minda yaguga, nthaka yauma; tirigu wawonongeka, vinyo watsopano watha, mitengo ya mafuta yauma. Onani mutuwo |