Yoweli 1:11 - Buku Lopatulika11 Gomani, akulima m'minda inu; lirani, akulima mpesa; chifukwa cha tirigu ndi barele; pakuti dzinthu za m'minda zatayika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Gomani, akulima m'minda inu; lirani, akulima mpesa; chifukwa cha tirigu ndi barele; pakuti dzinthu za m'minda zatayika. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tayani mtima, inu alimi, lirani, inu olima mphesa, chifukwa tirigu ndi barele, ndi zonse zam'minda zalephera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Khalani ndi nkhawa, inu alimi, lirani mofuwula inu alimi a mphesa; imvani chisoni chifukwa cha tirigu ndi barele, pakuti zokolola za mʼmunda zawonongeka. Onani mutuwo |