Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yoweli 1:8 - Buku Lopatulika

8 Lirani ngati namwali wodzimangira m'chuuno chiguduli, chifukwa cha mwamuna wa unamwali wake.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Lirani ngati namwali wodzimangira m'chuuno chiguduli, chifukwa cha mwamuna wa unamwali wake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Inu anthu, lirani kwambiri ngati namwali wovala chiguduli. Wolira chifukwa cha imfa ya mnyamata wofuna kumkwatira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Lirani ngati namwali wovala chiguduli, chifukwa cha mwamuna wa utsikana wake.

Onani mutuwo Koperani




Yoweli 1:8
13 Mawu Ofanana  

wosiya bwenzi la ubwana wake, naiwala chipangano cha Mulungu wake.


Ndipo tsiku limenelo Ambuye, Yehova wa makamu, anaitana kulira, ndi kugwa misozi, ndi kumeta, ndi kuvala chiguduli m'chuuno;


Nthunthumirani, inu akazi, amene mulinkukhala phee; vutidwani, inu osasamalira, vulani mukhale maliseche, nimumange chiguduli m'chuuno mwanu.


Kodi kuyambira tsopano sudzafuulira kwa Ine, Atate wanga, wotsogolera ubwana wanga ndinu?


M'njira za Ziyoni mulira posoweka akudzera msonkhano; pa zipata zake zonse papasuka; ansembe ake onse ausa moyo; anamwali ake asautsidwa; iye mwini namva zowawa.


Ndipo ndidzasanduliza zikondwerero zanu zikhale maliro, ndi nyimbo zanu zikhale za maliro, ndi kufikitsa ziguduli m'chuuno monse, ndi mpala pamutu uliwonse; nadzakhala ngati maliro a mwana mmodzi yekha, ndi chitsiriziro chake ngati tsiku lowawa.


Ndipo sanatero kodi wina womtsalira mzimu? Ndipo winayo anatero bwanji? Anatero pofuna mbeu ya Mulungu. Koma sungani mzimu wanu; ndipo asamchitire monyenga mkazi wa ubwana wake ndi mmodzi yense.


Nanga tsono achuma inu, lirani ndi kuchema chifukwa cha masautso anu akudza pa inu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa