Yoweli 1:3 - Buku Lopatulika3 Mufotokozere ana anu ichi, ndi ana anu afotokozere ana ao, ndi ana ao afotokozere mbadwo wina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Mufotokozere ana anu ichi, ndi ana anu afotokozere ana ao, ndi ana ao afotokozere mbadwo wina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Muŵauze ana anu, iwowo auze ana ao, ndipo anawo aziwuzanso ana ao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Muwafotokozere ana anu, ndipo ana anuwo afotokozere ana awo, ndipo ana awo adzafotokozere mʼbado winawo. Onani mutuwo |