Yoweli 1:19 - Buku Lopatulika19 Ndifuulira kwa Inu Yehova, pakuti moto wapsereza mabusa a m'chipululu, ndi malawi a moto anatentha mitengo yonse yakuthengo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndifuulira kwa Inu Yehova, pakuti moto wapsereza mabusa a m'chipululu, ndi malawi a moto anatentha mitengo yonse ya kuthengo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Ndikulira kwa Inu Chauta, pakuti moto wapsereza mabusa akuthengo, ndipo malaŵi a moto apsereza mitengo yonse yam'tchire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Kwa Inu Yehova ndilirira, pakuti moto wapsereza msipu wakuthengo, malawi amoto apsereza mitengo yonse ya mʼtchire. Onani mutuwo |