Yoweli 1:20 - Buku Lopatulika20 Inde nyama zakuthengo zilira kwa Inu; pakuti mitsinje yamadzi yaphwa, ndi moto wapsereza mabusa a m'chipululu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Inde nyama zakuthengo zilira kwa Inu; pakuti mitsinje yamadzi yaphwa, ndi moto wapsereza mabusa a m'chipululu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Nazonso nyama zakuthengo zikulira kwa Inu, chifukwa timitsinje tonse taphwa, ndipo moto wapsereza mabusa akuthengo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ngakhale nyama zakuthengo zikulirira Inu; timitsinje tonse taphwa ndipo moto wapsereza msipu wa kuthengo. Onani mutuwo |