Yoweli 1:17 - Buku Lopatulika17 Mbeu zaola pansi pa zibuluma zao; zosungiramo zaonongeka, nkhokwe zapasuka; pakuti tirigu wakwinyata. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Mbeu zaola pansi pa zibuluma zao; zosungiramo zaonongeka, nkhokwe zapasuka; pakuti tirigu wakwinyata. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Mbeu zakongonyala, poti pansi mpouma. Nyumba zosungiramo dzinthu zaonongeka, nkhokwe zapasuka, popeza kuti zokolola palibe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Mbewu zikunyala poti pansi ndi powuma. Nyumba zosungiramo zinthu zawonongeka; nkhokwe zapasuka popeza tirigu wauma. Onani mutuwo |