Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yoswa 3:2 - Buku Lopatulika

2 Ndipo kunali atapita masiku atatu, akapitao anapita pakati pa chigono;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo kunali atapita masiku atatu, akapitao anapita pakati pa chigono;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Patapita masiku atatu, atsogoleri adakayendera zithando zonse,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Patatha masiku atatu, atsogoleri anayendera misasa yonse,

Onani mutuwo Koperani




Yoswa 3:2
2 Mawu Ofanana  

nalamulira anthu, ndi kuti, Mukadzaona likasa la chipangano la Yehova Mulungu wanu, ndi ansembe Aleviwo atalisenza, pamenepo muchoke kwanu ndi kulitsata.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa