Yoswa 1:2 - Buku Lopatulika2 Mose mtumiki wanga wafa; tauka tsono, nuoloke Yordani uyu, iwe ndi anthu awa onse, kulowa m'dzikomo ndilikuwapatsa, ndiwo ana a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Mose mtumiki wanga wafa; tauka tsono, nuoloke Yordani uyu, iwe ndi anthu awa onse, kulowa m'dzikomo ndilikuwapatsa, ndiwo ana a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 “Mose, mtumiki wanga, wafa. Tsono iwe, konzeka tsopano pamodzi ndi Aisraele onseŵa, muwoloke mtsinje wa Yordaniwu, ndipo muloŵe m'dziko limene ndikuŵapatsalo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 “Mose mtumiki wanga wamwalira. Ndipo iwe ndi anthu onsewa, tsopano konzekani kuwoloka mtsinje wa Yorodani kupita ku dziko limene ndiwapatse Aisraeli onse. Onani mutuwo |