Yoswa 1:3 - Buku Lopatulika3 Pali ponse phazi lanu lidzapondapo ndinakupatsani, monga ndinanena ndi Mose. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pali ponse phazi lanu lidzapondapo ndinakupatsani, monga ndinanena ndi Mose. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Paliponse pamene muponde phazi lanu, ndakupatsani inu, monga momwe ndidalonjezera Mose. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Paliponse pamene phazi lanu liponde, ndikupatsani monga momwe ndinalonjezera Mose. Onani mutuwo |