Yona 4:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo tsopano, Yehova, mundichotseretu moyo wanga, kundikomera ine kufa, osakhala ndi moyo ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo tsopano, Yehova, mundichotseretu moyo wanga, kundikomera ine kufa, osakhala ndi moyo ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndiye tsono Inu Chauta, ndapota nanu, ingondiphani basi. Nkhwabwino kuti ndife kupambana kukhala moyo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Ndipo tsopano, Inu Yehova, ingondiphani basi, pakuti ndi bwino kuti ndife kupambana nʼkukhala ndi moyo.” Onani mutuwo |