Yohane 9:5 - Buku Lopatulika5 Pakukhala Ine m'dziko lapansi, ndili kuunika kwa dziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakukhala Ine m'dziko lapansi, ndili kuunika kwa dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pamene ndili pansi pano, ndine kuŵala kounikira anthu onse.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Pamene Ine ndili mʼdziko lapansi, Ine ndine kuwunika kwa dziko lapansi.” Onani mutuwo |