Yohane 9:6 - Buku Lopatulika6 Pamene ananena izi, analavula pansi, nakanda thope ndi malovuwo, napaka thopelo m'maso, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Pamene ananena izi, analavula pansi, nakanda thope ndi malovuwo, napaka thopelo m'maso, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Atanena zimenezi, Yesu adalavulira malovu pansi, nakanda thope ndi malovuwo. Kenaka adapaka thopelo m'maso mwa munthuyo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Atanena izi, Iye anathira malovu pansi ndi kukanda dothi, napaka matopewo mʼmaso a munthuyo. Onani mutuwo |