Yohane 9:4 - Buku Lopatulika4 Tiyenera kugwira ntchito za Iye wondituma Ine, pokhala pali msana; ukudza usiku pamene palibe munthu angakhoze kugwira ntchito. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Tiyenera kugwira ntchito za Iye wondituma Ine, pokhala pali msana; ukudza usiku pamene palibe munthu angakhoze kugwira ntchito. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Kukali usana tizigwira ntchito za Atate amene adandituma. Usiku ukudza pamene munthu sangathe kugwira ntchito. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ife tiyenera kugwira ntchito za Iye amene anandituma kukanali masana. Usiku ukubwera, pamene wina aliyense sadzagwira ntchito. Onani mutuwo |