Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Yohane 9:40 - Buku Lopatulika

40 Ndipo Afarisi ena akukhala ndi Iye anamva izi, nati kwa Iye, Kodi ifenso ndife osaona?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

40 Ndipo Afarisi ena akukhala ndi Iye anamva izi, nati kwa Iye, Kodi ifenso ndife osaona?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

40 Afarisi ena amene anali pafupi naye, atamva zimenezi adamufunsa kuti, “Kodi monga ifenso ndife akhungu?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

40 Afarisi ena amene anali pafupi naye anamva akunena izi ndipo anafunsa kuti, “Chiyani? Kodi ndife osaonanso?”

Onani mutuwo Koperani




Yohane 9:40
8 Mawu Ofanana  

Anayankha nati kwa iye, Wabadwa iwe konse m'zoipa, ndipo iwe utiphunzitse ife kodi? Ndipo anamtaya kunja.


Yesu anati kwa iwo, Mukadakhala osaona simukadakhala nalo tchimo; koma tsopano munena, kuti, Tipenya: tchimo lanu likhala.


Chifukwa unena kuti ine ndine wolemera, ndipo chuma ndili nacho, osasowa kanthu; ndipo sudziwa kuti ndiwe watsoka, ndi wochititsa chifundo, ndi wosauka, ndi wakhungu, ndi wausiwa;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa