Yohane 9:41 - Buku Lopatulika41 Yesu anati kwa iwo, Mukadakhala osaona simukadakhala nalo tchimo; koma tsopano munena, kuti, Tipenya: tchimo lanu likhala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201441 Yesu anati kwa iwo, Mukadakhala osaona simukadakhala nalo tchimo; koma tsopano munena, kuti, Tipenya: tchimo lanu likhala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa41 Yesu adati, “Mukadakhala akhungu, bwenzi mulibe mlandu. Koma chifukwa mukuti, ‘Tikupenya,’ ndiye kuti mlandu wanu ulipobe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero41 Yesu anati, “Mukanakhala osaona, simukanachimwa; koma tsopano popeza mukuti mumaona, ndinu ochimwabe.” Onani mutuwo |